Ekisodo 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tamvera! Ine ndidzatsogola kukaima pathanthwe ku Horebe.* Kumeneko ukamenye thanthwelo, ndipo padzatuluka madzi amene anthu adzamwa.”+ Chotero Mose anachitadi zomwezo, pamaso pa akulu a Isiraeli, Numeri 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mose atatero, anakweza dzanja lake n’kumenya thanthwelo kawiri ndi ndodo yake. Pamenepo madzi ambiri anayamba kutuluka, ndipo khamu lonselo linayamba kumwa madziwo limodzi ndi ziweto zawo.+
6 Tamvera! Ine ndidzatsogola kukaima pathanthwe ku Horebe.* Kumeneko ukamenye thanthwelo, ndipo padzatuluka madzi amene anthu adzamwa.”+ Chotero Mose anachitadi zomwezo, pamaso pa akulu a Isiraeli,
11 Mose atatero, anakweza dzanja lake n’kumenya thanthwelo kawiri ndi ndodo yake. Pamenepo madzi ambiri anayamba kutuluka, ndipo khamu lonselo linayamba kumwa madziwo limodzi ndi ziweto zawo.+