Ekisodo 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tamvera! Ine ndidzatsogola kukaima pathanthwe ku Horebe.* Kumeneko ukamenye thanthwelo, ndipo padzatuluka madzi amene anthu adzamwa.”+ Chotero Mose anachitadi zomwezo, pamaso pa akulu a Isiraeli, Deuteronomo 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mungaiwale amene anakuyendetsani m’chipululu chachikulu ndi chochititsa mantha,+ chokhala ndi njoka zapoizoni,+ zinkhanira ndiponso dziko louma lopanda madzi. Amenenso anakutulutsirani madzi pamwala wolimba ngati nsangalabwi.+ 1 Akorinto 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ndipo onse anamwa chakumwa chimodzimodzi chauzimu.+ Pakuti anali kumwa pathanthwe lauzimu+ limene linali kuwatsatira, ndipo thanthwelo+ linatanthauza Khristu.+
6 Tamvera! Ine ndidzatsogola kukaima pathanthwe ku Horebe.* Kumeneko ukamenye thanthwelo, ndipo padzatuluka madzi amene anthu adzamwa.”+ Chotero Mose anachitadi zomwezo, pamaso pa akulu a Isiraeli,
15 Mungaiwale amene anakuyendetsani m’chipululu chachikulu ndi chochititsa mantha,+ chokhala ndi njoka zapoizoni,+ zinkhanira ndiponso dziko louma lopanda madzi. Amenenso anakutulutsirani madzi pamwala wolimba ngati nsangalabwi.+
4 ndipo onse anamwa chakumwa chimodzimodzi chauzimu.+ Pakuti anali kumwa pathanthwe lauzimu+ limene linali kuwatsatira, ndipo thanthwelo+ linatanthauza Khristu.+