Numeri 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mose atatero, anakweza dzanja lake n’kumenya thanthwelo kawiri ndi ndodo yake. Pamenepo madzi ambiri anayamba kutuluka, ndipo khamu lonselo linayamba kumwa madziwo limodzi ndi ziweto zawo.+
11 Mose atatero, anakweza dzanja lake n’kumenya thanthwelo kawiri ndi ndodo yake. Pamenepo madzi ambiri anayamba kutuluka, ndipo khamu lonselo linayamba kumwa madziwo limodzi ndi ziweto zawo.+