Ezekieli 16:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Inenso ndidzakubwezera mogwirizana ndi zochita zako,+ chifukwa unanyoza lumbiro pophwanya pangano langa.+ Aheberi 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ‘Koma pangano+ limeneli si lofanana ndi limene ndinapangana ndi makolo awo pamene ndinagwira dzanja lawo kuti ndiwatulutse m’dziko la Iguputo,+ chifukwa iwo sanapitirize kusunga pangano+ langalo moti ndinasiya kuwasamalira,’ watero Yehova.”+
59 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Inenso ndidzakubwezera mogwirizana ndi zochita zako,+ chifukwa unanyoza lumbiro pophwanya pangano langa.+
9 ‘Koma pangano+ limeneli si lofanana ndi limene ndinapangana ndi makolo awo pamene ndinagwira dzanja lawo kuti ndiwatulutse m’dziko la Iguputo,+ chifukwa iwo sanapitirize kusunga pangano+ langalo moti ndinasiya kuwasamalira,’ watero Yehova.”+