Yeremiya 31:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “Koma pangano limeneli si lofanana ndi limene ndinapangana ndi makolo awo pamene ndinagwira dzanja lawo kuti ndiwatulutse m’dziko la Iguputo.+ ‘Pangano langa limenelo analiphwanya+ ngakhale kuti ine ndinali mwamuna wawo,’+ watero Yehova.”
32 “Koma pangano limeneli si lofanana ndi limene ndinapangana ndi makolo awo pamene ndinagwira dzanja lawo kuti ndiwatulutse m’dziko la Iguputo.+ ‘Pangano langa limenelo analiphwanya+ ngakhale kuti ine ndinali mwamuna wawo,’+ watero Yehova.”