Deuteronomo 29:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 kuti muchite pangano+ ndi Yehova Mulungu wanu mwa kulumbira, pangano limene Yehova Mulungu wanu akuchita nanu lero.+ Yeremiya 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo adzanena kuti: “Anauchitira zimenezi chifukwa chakuti anthu a mumzindawu anasiya pangano la Yehova Mulungu wawo+ ndi kuyamba kulambira milungu ina ndi kuitumikira.”’+
12 kuti muchite pangano+ ndi Yehova Mulungu wanu mwa kulumbira, pangano limene Yehova Mulungu wanu akuchita nanu lero.+
9 Ndipo adzanena kuti: “Anauchitira zimenezi chifukwa chakuti anthu a mumzindawu anasiya pangano la Yehova Mulungu wawo+ ndi kuyamba kulambira milungu ina ndi kuitumikira.”’+