29Awa ndi mawu a pangano limene Yehova analamula Mose kuti achite ndi ana a Isiraeli m’dziko la Mowabu, kuwonjezera pa pangano limene anachita nawo ku Horebe.+
29 “Zinthu zobisika+ ndi za Yehova Mulungu wathu, koma zinthu zoululidwa+ ndi zathu ndi ana athu mpaka kalekale, kuti titsatire mawu onse a chilamulo ichi.+