-
Salimo 78:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Mulungu anaika chikumbutso pakati pa ana a Yakobo,+
Iye anaika chilamulo mu Isiraeli,+
Zinthu zimene analamula makolo athu,+
Kuti auze ana awo.+
-