Ekisodo 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo Mose anatenga magaziwo ndi kuwaza anthuwo,+ ndipo anati: “Awa ndiwo magazi okhazikitsira pangano+ limene Yehova wapangana nanu mwa mawu onsewa.” Levitiko 26:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ndipo ndidzakumbukira m’malo mwawo pangano limene ndinachita ndi makolo awo,+ amene ndinawatulutsa m’dziko la Iguputo, anthu a mitundu ina akuona.+ Ndidzachita zimenezi kuti ndiwasonyeze kuti ndine Mulungu wawo. Ine ndine Yehova.’” Deuteronomo 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova Mulungu wathu anachita nafe pangano ku Horebe.+
8 Pamenepo Mose anatenga magaziwo ndi kuwaza anthuwo,+ ndipo anati: “Awa ndiwo magazi okhazikitsira pangano+ limene Yehova wapangana nanu mwa mawu onsewa.”
45 Ndipo ndidzakumbukira m’malo mwawo pangano limene ndinachita ndi makolo awo,+ amene ndinawatulutsa m’dziko la Iguputo, anthu a mitundu ina akuona.+ Ndidzachita zimenezi kuti ndiwasonyeze kuti ndine Mulungu wawo. Ine ndine Yehova.’”