Mika 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Dzanja lanu lidzakhala pamwamba pa adani anu,+ ndipo adani anu onse adzaphedwa.”+ Aroma 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma chifukwa chakuti ndiwe wosafuna kusintha khalidwe+ ndiponso wa mtima wosalapa,+ ukudzisungira mkwiyo wa Mulungu.+ Mulungu adzasonyeza mkwiyo+ umenewu pa tsiku loulula+ chiweruzo chake cholungama.+ 2 Petulo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+
5 Koma chifukwa chakuti ndiwe wosafuna kusintha khalidwe+ ndiponso wa mtima wosalapa,+ ukudzisungira mkwiyo wa Mulungu.+ Mulungu adzasonyeza mkwiyo+ umenewu pa tsiku loulula+ chiweruzo chake cholungama.+
9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+