Salimo 79:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atsanula magazi awo ngati madziKuzungulira Yerusalemu yense, ndipo palibe wowaika m’manda.+ Chivumbulutso 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndipo anapondaponda mopondera mphesamo kunja kwa mzinda,+ ndipo magazi anatuluka m’choponderamo mphesacho mpaka kufika m’zibwano za mahatchi,+ n’kuyenderera mtunda wa masitadiya 1,600.*+
20 Ndipo anapondaponda mopondera mphesamo kunja kwa mzinda,+ ndipo magazi anatuluka m’choponderamo mphesacho mpaka kufika m’zibwano za mahatchi,+ n’kuyenderera mtunda wa masitadiya 1,600.*+