Genesis 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense wokhetsa magazi a munthu, nayenso magazi ake adzakhetsedwa ndi munthu,+ chifukwa Mulungu anapanga munthu m’chifaniziro chake. Ekisodo 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Amene wamenya munthu mpaka munthuyo kufa ayenera kuphedwa ndithu.+ Salimo 79:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atsanula magazi awo ngati madziKuzungulira Yerusalemu yense, ndipo palibe wowaika m’manda.+
6 Aliyense wokhetsa magazi a munthu, nayenso magazi ake adzakhetsedwa ndi munthu,+ chifukwa Mulungu anapanga munthu m’chifaniziro chake.