Salimo 74:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 74 Inu Mulungu, n’chifukwa chiyani mwatitaya?+N’chifukwa chiyani mkwiyo wanu ukuyakira nkhosa zimene mukuweta?+ Salimo 85:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kodi mupitiriza kutikwiyira mpaka kalekale?+Kodi mudzasonyeza mkwiyo wanu ku mibadwomibadwo?+ Yesaya 64:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu Yehova musatikwiyire kwambiri,+ ndipo musakumbukire zolakwa zathu kwamuyaya.+ Chonde, kumbukirani kuti tonsefe ndife anthu anu.+
74 Inu Mulungu, n’chifukwa chiyani mwatitaya?+N’chifukwa chiyani mkwiyo wanu ukuyakira nkhosa zimene mukuweta?+
9 Inu Yehova musatikwiyire kwambiri,+ ndipo musakumbukire zolakwa zathu kwamuyaya.+ Chonde, kumbukirani kuti tonsefe ndife anthu anu.+