Salimo 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 N’chifukwa chiyani inu Yehova mukuima kutali?+N’chifukwa chiyani mukubisala pa nthawi ya masautso?+ Salimo 44:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Nyamukani. N’chifukwa chiyani mukugonabe, inu Yehova?+Dzukani. Musatitaye kwamuyaya.+ Maliro 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 N’chifukwa chiyani mwatiiwala kwamuyaya+ ndi kutisiya kwa masiku ambiri?+
10 N’chifukwa chiyani inu Yehova mukuima kutali?+N’chifukwa chiyani mukubisala pa nthawi ya masautso?+