Salimo 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nyamukani, inu Yehova, mu mkwiyo wanu.+Imirirani ndi kukhaulitsa amene andisonyeza mkwiyo ndi kundichitira zoipa.+Dzukani ndi kundithandiza,+ pakuti mwalamula kuti chiweruzo chiperekedwe.+ Salimo 78:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Pamenepo Yehova anagalamuka ngati akudzuka kutulo,+Ngati munthu wamphamvu amene akugalamuka pambuyo pomwa vinyo wambiri.+
6 Nyamukani, inu Yehova, mu mkwiyo wanu.+Imirirani ndi kukhaulitsa amene andisonyeza mkwiyo ndi kundichitira zoipa.+Dzukani ndi kundithandiza,+ pakuti mwalamula kuti chiweruzo chiperekedwe.+
65 Pamenepo Yehova anagalamuka ngati akudzuka kutulo,+Ngati munthu wamphamvu amene akugalamuka pambuyo pomwa vinyo wambiri.+