Salimo 44:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Nyamukani. N’chifukwa chiyani mukugonabe, inu Yehova?+Dzukani. Musatitaye kwamuyaya.+ Salimo 73:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Inu Yehova, anthu amenewa ali ngati maloto amene aiwalika podzuka.+Choncho pamene mukuimirira mudzawakana mochititsa manyazi.+ Yesaya 51:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Dzuka! Dzuka! Vala mphamvu,+ iwe dzanja la Yehova!+ Dzuka ngati masiku akale, ngati m’mibadwo yakalekale.+ Kodi si iwe amene unaphwanyaphwanya Rahabi,+ amene unabaya* chilombo cha m’nyanja?+
20 Inu Yehova, anthu amenewa ali ngati maloto amene aiwalika podzuka.+Choncho pamene mukuimirira mudzawakana mochititsa manyazi.+
9 Dzuka! Dzuka! Vala mphamvu,+ iwe dzanja la Yehova!+ Dzuka ngati masiku akale, ngati m’mibadwo yakalekale.+ Kodi si iwe amene unaphwanyaphwanya Rahabi,+ amene unabaya* chilombo cha m’nyanja?+