Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 6:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiyeno Gidiyoni anayankha kuti: “Pepani mbuyanga, koma ngati Yehova ali ndi ife, n’chifukwa chiyani zonsezi zatigwera?+ Nanga ntchito zake zodabwitsa zija,+ zimene makolo athu anatisimbira zili kuti?+ Iwo anatiuza kuti, ‘Yehova ndiye anatitulutsa mu Iguputo.’+ Koma tsopano Yehova watisiya,+ ndipo watipereka m’manja mwa Amidiyani.”

  • Nehemiya 9:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno munaonetsa Farao zizindikiro ndi zozizwitsa zomukhaulitsa pamodzi ndi atumiki ake onse ndi anthu onse okhala m’dziko lake.+ Munatero chifukwa munadziwa kuti iwo anachita zinthu modzikuza+ kwa makolo athu. Pamenepo munadzipangira dzina+ kufikira lero.

  • Salimo 44:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Inu Mulungu, ife tamva ndi makutu athu,

      Makolo athu anatifotokozera+

      Ntchito zimene inu munachita m’masiku awo,+

      M’masiku akale.+

  • Salimo 106:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Amene anachita zodabwitsa m’dziko la Hamu,+

      Amene anachita zochititsa mantha pa Nyanja Yofiira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena