Salimo 89:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwaphwanya Rahabi*+ ndi kumuchititsa kukhala ngati munthu amene waphedwa.+Mwabalalitsa adani anu ndi dzanja lanu lamphamvu.+ Yesaya 53:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Kodi ndani wakhulupirira zimene ife tamva?+ Ndipo kodi dzanja la Yehova+ laonetsedwa kwa ndani?+ Luka 1:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Wachita zamphamvu ndi dzanja lake,+ wabalalitsira kutali odzikweza m’zolinga za mitima yawo.+
10 Mwaphwanya Rahabi*+ ndi kumuchititsa kukhala ngati munthu amene waphedwa.+Mwabalalitsa adani anu ndi dzanja lanu lamphamvu.+