Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 14:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Tambasula dzanja lako ndi kuloza panyanja,+ kuti madzi abwerere ndi kumiza Aiguputo, magaleta awo ankhondo ndi asilikali awo apamahatchi.”

  • Salimo 87:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ine ndidzatchula Rahabi*+ ndi Babulo+ monga ena mwa amene akundidziwa.

      Ponena za Filisitiya,+ Turo ndi Kusi ine ndidzati:

      “Amenewa anabadwira m’Ziyoni.”+

  • Yesaya 30:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Aiguputo ndi anthu achabechabe ndipo sadzakuthandizani chilichonse.+ Choncho ndinawatcha kuti, “Rahabi.+ Iwo sadzachita chilichonse.”

  • Yesaya 51:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Dzuka! Dzuka! Vala mphamvu,+ iwe dzanja la Yehova!+ Dzuka ngati masiku akale, ngati m’mibadwo yakalekale.+ Kodi si iwe amene unaphwanyaphwanya Rahabi,+ amene unabaya* chilombo cha m’nyanja?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena