Salimo 87:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzaika Rahabi* ndi Babulo mʼgulu la amene+ akundidziwa.Filisitiya, Turo ndi Kusi alinso mʼgulu la amene akundidziwa. Ine ndidzati: “Amenewa anabadwira mʼZiyoni.”
4 Ndidzaika Rahabi* ndi Babulo mʼgulu la amene+ akundidziwa.Filisitiya, Turo ndi Kusi alinso mʼgulu la amene akundidziwa. Ine ndidzati: “Amenewa anabadwira mʼZiyoni.”