2 Samueli 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Davide anayamba kutonthoza mkazi wake Bati-seba.+ Kuwonjezera apo, analowa kwa iye ndipo anagona naye. Patapita nthawi, anamuberekera mwana wamwamuna+ amene anamutcha dzina lakuti Solomo.*+ Yehova anam’konda mwana ameneyu.+ Agalatiya 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chotero abale, ife ndife ana a mkazi waufulu,+ osati a mdzakazi.+
24 Ndiyeno Davide anayamba kutonthoza mkazi wake Bati-seba.+ Kuwonjezera apo, analowa kwa iye ndipo anagona naye. Patapita nthawi, anamuberekera mwana wamwamuna+ amene anamutcha dzina lakuti Solomo.*+ Yehova anam’konda mwana ameneyu.+