Yohane 8:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho ngati Mwana wakumasulani, mudzakhaladi omasuka.+ Agalatiya 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zoonadi abale, munaitanidwa kuti mukhale aufulu,+ musayese ngakhale pang’ono kugwiritsa ntchito ufulu umenewu polimbikitsira zilakolako za thupi,+ koma tumikiranani mwachikondi.+
13 Zoonadi abale, munaitanidwa kuti mukhale aufulu,+ musayese ngakhale pang’ono kugwiritsa ntchito ufulu umenewu polimbikitsira zilakolako za thupi,+ koma tumikiranani mwachikondi.+