1 Akorinto 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma muzikhalabe osamala kuti ufulu wanuwo usakhale chopunthwitsa kwa ofooka.+ 1 Petulo 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Khalani mfulu,+ koma ufulu wanu usakhale ngati chophimbira zoipa,+ koma monga akapolo a Mulungu.+ 2 Petulo 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamene akuwalonjeza ufulu,+ eni akewo ndi akapolo a khalidwe loipa.+ Pakuti aliyense amene wagonjetsedwa, amakhala kapolo kwa womugonjetsayo.+
19 Pamene akuwalonjeza ufulu,+ eni akewo ndi akapolo a khalidwe loipa.+ Pakuti aliyense amene wagonjetsedwa, amakhala kapolo kwa womugonjetsayo.+