1 Mbiri 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ku Yerusalemu+ iye anabereka ana awa: Simeya,+ Sobabu,+ Natani,+ ndi Solomo,+ ana anayi obadwa kwa Bati-seba+ mwana wamkazi wa Amiyeli.+ 1 Mbiri 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Taona, udzabala mwana.+ Mwana ameneyo adzakhala munthu wabata, ndipo ndidzam’patsa mpumulo pakati pa adani ake onse omuzungulira.+ N’chifukwa chake dzina lake adzakhala Solomo,*+ ndipo m’masiku ake ndidzakhazikitsa mtendere+ ndi bata pa Isiraeli. 1 Mbiri 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo pa ana anga onse (pakuti Yehova wandipatsa ana ambiri)+ anasankha mwana wanga Solomo+ kuti akhale pampando wachifumu+ wa ufumu wa Yehova, kuti alamulire Isiraeli. Mateyu 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Jese anabereka mfumu+ Davide.+ Davide anabereka Solomo,+ yemwe mayi ake anali mkazi wa Uriya.
5 Ku Yerusalemu+ iye anabereka ana awa: Simeya,+ Sobabu,+ Natani,+ ndi Solomo,+ ana anayi obadwa kwa Bati-seba+ mwana wamkazi wa Amiyeli.+
9 Taona, udzabala mwana.+ Mwana ameneyo adzakhala munthu wabata, ndipo ndidzam’patsa mpumulo pakati pa adani ake onse omuzungulira.+ N’chifukwa chake dzina lake adzakhala Solomo,*+ ndipo m’masiku ake ndidzakhazikitsa mtendere+ ndi bata pa Isiraeli.
5 Ndipo pa ana anga onse (pakuti Yehova wandipatsa ana ambiri)+ anasankha mwana wanga Solomo+ kuti akhale pampando wachifumu+ wa ufumu wa Yehova, kuti alamulire Isiraeli.