1 Mbiri 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzamukhazikitsa iye kukhala woyang’anira nyumba yanga+ ndi ufumu wanga+ mpaka kalekale, ndipo mpando wake wachifumu+ sudzatha mpaka kalekale.”’” 2 Mbiri 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Solomo atamva zimenezi anauza Mulungu kuti: “Inu ndinu amene mwasonyeza kukoma mtima kosatha kwa Davide bambo anga,+ ndipo mwandiika kukhala mfumu m’malo mwake.+
14 Ndidzamukhazikitsa iye kukhala woyang’anira nyumba yanga+ ndi ufumu wanga+ mpaka kalekale, ndipo mpando wake wachifumu+ sudzatha mpaka kalekale.”’”
8 Solomo atamva zimenezi anauza Mulungu kuti: “Inu ndinu amene mwasonyeza kukoma mtima kosatha kwa Davide bambo anga,+ ndipo mwandiika kukhala mfumu m’malo mwake.+