2 Samueli 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano mtumiki wanga Davide ukamuuze kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Ine ndinakutenga kubusa, kumene unali kusamalira nkhosa+ kuti ukhale mtsogoleri+ wa anthu anga Aisiraeli. Salimo 89:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndidzamusonyeza kukoma mtima kwanga kosatha mpaka kalekale,+Ndipo pangano limene ndinachita naye silidzaphwanyidwa.+
8 Tsopano mtumiki wanga Davide ukamuuze kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Ine ndinakutenga kubusa, kumene unali kusamalira nkhosa+ kuti ukhale mtsogoleri+ wa anthu anga Aisiraeli.
28 Ndidzamusonyeza kukoma mtima kwanga kosatha mpaka kalekale,+Ndipo pangano limene ndinachita naye silidzaphwanyidwa.+