Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kuyambira kale+ pamene Sauli anali mfumu yathu, inuyo munali kutsogolera Isiraeli polowa ndi potuluka.+ Ndipo Yehova anakuuzani kuti, ‘Udzaweta+ anthu anga Aisiraeli ndipo udzakhala mtsogoleri+ wa Isiraeli.’”

  • 2 Samueli 6:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Poyankha, Davide anauza Mikala kuti: “Ine ndinali kusangalala pamaso pa Yehova amene anandisankha kuti ndikhale mtsogoleri+ wa anthu a Yehova, Aisiraeli, m’malo mwa bambo ako ndi banja lawo lonse, ndipo ndidzasangalala pamaso pa Yehova.+

  • 1 Mbiri 28:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Komabe, m’nyumba yonse ya bambo anga+ Yehova Mulungu wa Isiraeli anasankha ineyo kuti ndikhale mfumu+ ya Isiraeli mpaka kalekale, popeza anasankha Yuda kuti akhale mtsogoleri.+ M’nyumba ya Yuda anasankhamo nyumba ya bambo anga.+ Pa ana a bambo anga+ anavomereza ineyo+ kuti ndikhale mfumu ya Isiraeli yense.

  • Salimo 78:71
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 71 Anamutenga kumene anali kuweta nkhosa zoyamwitsa,+

      Anamutenga kuti akhale m’busa wa ana a Yakobo amene ndi anthu ake,+

      Ndi Isiraeli, amene ndi cholowa chake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena