Genesis 49:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, kufikira Silo*+ atabwera. Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+ 1 Mbiri 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chifukwa chakuti Yuda+ anali wamphamvu pakati pa abale ake, mwa iye munachokera mtsogoleri,+ koma udindo wa woyamba kubadwa unali wa Yosefe.+ Salimo 60:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Giliyadi ndi wanga ndipo Manase ndi wanganso.+Efuraimu ndi malo otetezeka a mtsogoleri amene ine ndamuika.Yuda ndi ndodo ya mtsogoleri wanga.+
10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, kufikira Silo*+ atabwera. Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+
2 Chifukwa chakuti Yuda+ anali wamphamvu pakati pa abale ake, mwa iye munachokera mtsogoleri,+ koma udindo wa woyamba kubadwa unali wa Yosefe.+
7 Giliyadi ndi wanga ndipo Manase ndi wanganso.+Efuraimu ndi malo otetezeka a mtsogoleri amene ine ndamuika.Yuda ndi ndodo ya mtsogoleri wanga.+