Genesis 49:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Madalitso a bambo ako adzapambana madalitso a mapiri amene adzakhalapo mpaka kalekale.+ Adzapambananso ulemerero wa zitunda zosatha.+ Madalitsowo adzakhalabe pamutu pa Yosefe, paliwombo pa wosankhidwa pakati pa abale ake.+
26 Madalitso a bambo ako adzapambana madalitso a mapiri amene adzakhalapo mpaka kalekale.+ Adzapambananso ulemerero wa zitunda zosatha.+ Madalitsowo adzakhalabe pamutu pa Yosefe, paliwombo pa wosankhidwa pakati pa abale ake.+