Mateyu 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Iwe Betelehemu+ wa m’dziko la Yuda, suli mzinda waung’ono kwambiri kwa olamulira a Yuda, chifukwa mwa iwe mudzatuluka wolamulira+ amene adzaweta+ anthu anga, Aisiraeli.’” Aheberi 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tonse tikudziwa kuti Ambuye wathu anatuluka m’fuko la Yuda,+ ndipo ponena za fuko limeneli Mose sanatchulepo chilichonse chokhudza ansembe.
6 ‘Iwe Betelehemu+ wa m’dziko la Yuda, suli mzinda waung’ono kwambiri kwa olamulira a Yuda, chifukwa mwa iwe mudzatuluka wolamulira+ amene adzaweta+ anthu anga, Aisiraeli.’”
14 Tonse tikudziwa kuti Ambuye wathu anatuluka m’fuko la Yuda,+ ndipo ponena za fuko limeneli Mose sanatchulepo chilichonse chokhudza ansembe.