Genesis 49:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, kufikira Silo*+ atabwera. Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+ Yesaya 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nthambi+ idzatuluka pachitsa cha Jese,+ ndipo mphukira+ yotuluka pamizu yake idzakhala yobereka zipatso.+ Mateyu 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yuda anabereka Perezi+ ndi Zera, ndipo mayi awo anali Tamara.Perezi anabereka Hezironi.+Hezironi anabereka Ramu.+ Luka 3:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 mwana wa Aminadabu,+mwana wa Arini,+mwana wa Hezironi,+mwana wa Perezi,+mwana wa Yuda,+ Mabuku a Chichewa (1974-2025) Tulukani Lowani Chichewa Tumizirani Ena Zimene Mumakonda Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania Zoyenera Kutsatira Nkhani Yosunga Chinsinsi Privacy Settings JW.ORG Lowani Tumizirani Ena Tumizirani Wina pa Imelo
10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, kufikira Silo*+ atabwera. Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+
11 Nthambi+ idzatuluka pachitsa cha Jese,+ ndipo mphukira+ yotuluka pamizu yake idzakhala yobereka zipatso.+
3 Yuda anabereka Perezi+ ndi Zera, ndipo mayi awo anali Tamara.Perezi anabereka Hezironi.+Hezironi anabereka Ramu.+ Luka 3:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 mwana wa Aminadabu,+mwana wa Arini,+mwana wa Hezironi,+mwana wa Perezi,+mwana wa Yuda,+