1 Mbiri 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ramu anabereka Aminadabu, Aminadabu+ anabereka Naasoni+ mtsogoleri wa ana a Yuda.