Numeri 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Chigawo cha mafuko atatu cha Yuda ndi asilikali awo, chizimanga msasa wawo kum’mawa kotulukira dzuwa. Mtsogoleri wa ana a Yuda ndi Naasoni,+ mwana wa Aminadabu. Luka 3:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 mwana wa Jese,+mwana wa Obedi,+mwana wa Boazi,+mwana wa Salimoni,+mwana wa Naasoni,+
3 “Chigawo cha mafuko atatu cha Yuda ndi asilikali awo, chizimanga msasa wawo kum’mawa kotulukira dzuwa. Mtsogoleri wa ana a Yuda ndi Naasoni,+ mwana wa Aminadabu.