Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 7:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Amene anapereka zopereka zake pa tsiku loyamba anali Naasoni,+ mwana wa Aminadabu, wa fuko la Yuda.

  • Numeri 10:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Choncho, a m’chigawo cha mafuko atatu cha ana a Yuda ndiwo anayamba kunyamuka m’magulu awo.+ Mtsogoleri wa asilikali awo anali Naasoni,+ mwana wa Aminadabu.

  • Rute 4:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Aminadabu+ anabereka Naasoni,+ Naasoni anabereka Salimoni,

  • 1 Mbiri 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ramu anabereka Aminadabu, Aminadabu+ anabereka Naasoni+ mtsogoleri wa ana a Yuda.

  • Mateyu 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ramu anabereka Aminadabu.

      Aminadabu anabereka Naasoni.+

      Naasoni anabereka Salimoni.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena