Numeri 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Chigawo cha mafuko atatu cha Yuda ndi asilikali awo, chizimanga msasa wawo kum’mawa kotulukira dzuwa. Mtsogoleri wa ana a Yuda ndi Naasoni,+ mwana wa Aminadabu. Rute 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Aminadabu+ anabereka Naasoni,+ Naasoni anabereka Salimoni, 1 Mbiri 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ramu anabereka Aminadabu, Aminadabu+ anabereka Naasoni+ mtsogoleri wa ana a Yuda. Luka 3:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 mwana wa Jese,+mwana wa Obedi,+mwana wa Boazi,+mwana wa Salimoni,+mwana wa Naasoni,+
3 “Chigawo cha mafuko atatu cha Yuda ndi asilikali awo, chizimanga msasa wawo kum’mawa kotulukira dzuwa. Mtsogoleri wa ana a Yuda ndi Naasoni,+ mwana wa Aminadabu.