Ekisodo 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Aroni anatenga Eliseba, mwana wamkazi wa Aminadabu, mlongo wake wa Naasoni,+ kukhala mkazi wake. Ndipo Eliseba anam’berekera Nadabu, Abihu, Eleazara ndi Itamara.+ 1 Mbiri 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ramu anabereka Aminadabu, Aminadabu+ anabereka Naasoni+ mtsogoleri wa ana a Yuda. Luka 3:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 mwana wa Aminadabu,+mwana wa Arini,+mwana wa Hezironi,+mwana wa Perezi,+mwana wa Yuda,+
23 Aroni anatenga Eliseba, mwana wamkazi wa Aminadabu, mlongo wake wa Naasoni,+ kukhala mkazi wake. Ndipo Eliseba anam’berekera Nadabu, Abihu, Eleazara ndi Itamara.+