Genesis 29:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anakhalanso ndi pakati pena n’kubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Tsopano nditamanda Yehova.” Choncho Leya anatcha mwanayo, Yuda.*+ Atabereka mwana ameneyu, anayamba waleka kubereka. Rute 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipo kudzera mwa ana amene Yehova adzakupatsa kwa mtsikanayu,+ nyumba yako ikhale ngati nyumba ya Perezi, amene Tamara anaberekera Yuda.”+ 1 Mbiri 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamara+ mpongozi wake ndiye anam’berekera Perezi+ ndi Zera. Ana onse a Yuda anali asanu. Mateyu 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yuda anabereka Perezi+ ndi Zera, ndipo mayi awo anali Tamara.Perezi anabereka Hezironi.+Hezironi anabereka Ramu.+
35 Anakhalanso ndi pakati pena n’kubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Tsopano nditamanda Yehova.” Choncho Leya anatcha mwanayo, Yuda.*+ Atabereka mwana ameneyu, anayamba waleka kubereka.
12 Ndipo kudzera mwa ana amene Yehova adzakupatsa kwa mtsikanayu,+ nyumba yako ikhale ngati nyumba ya Perezi, amene Tamara anaberekera Yuda.”+
3 Yuda anabereka Perezi+ ndi Zera, ndipo mayi awo anali Tamara.Perezi anabereka Hezironi.+Hezironi anabereka Ramu.+