Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 38:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Koma mwanayo anabweza dzanja lake. Nthawi yomweyo m’bale wake anatuluka, moti mzambayo anafuula kuti: “Ndiye chiyani wachitachi? Bwanji ukuchita kung’amba wekha njira?” N’chifukwa chake anamutcha dzina lakuti Perezi.*+

  • Numeri 26:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Choncho ana aamuna a Yuda mwa mabanja awo anali awa: Shela+ amene anali kholo la banja la Ashela, Perezi+ amene anali kholo la banja la Aperezi, ndi Zera+ amene anali kholo la banja la Azera.

  • 1 Mbiri 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Tamara+ mpongozi wake ndiye anam’berekera Perezi+ ndi Zera. Ana onse a Yuda anali asanu.

  • Mateyu 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Yuda anabereka Perezi+ ndi Zera, ndipo mayi awo anali Tamara.

      Perezi anabereka Hezironi.+

      Hezironi anabereka Ramu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena