Genesis 38:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma mwanayo anabweza dzanja lake. Nthawi yomweyo m’bale wake anatuluka, moti mzambayo anafuula kuti: “Ndiye chiyani wachitachi? Bwanji ukuchita kung’amba wekha njira?” N’chifukwa chake anamutcha dzina lakuti Perezi.*+ Genesis 46:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Yuda+ anali Ere,+ Onani,+ Shela,+ Perezi,+ ndi Zera.+ Komabe, Ere ndi Onani anafera kudziko la Kanani.+ Ana a Perezi anali Hezironi+ ndi Hamuli.+ Rute 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano uwu ndiwo mzere wa mbadwa za Perezi:+ Perezi anabereka Hezironi,+ Mateyu 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yuda anabereka Perezi+ ndi Zera, ndipo mayi awo anali Tamara.Perezi anabereka Hezironi.+Hezironi anabereka Ramu.+
29 Koma mwanayo anabweza dzanja lake. Nthawi yomweyo m’bale wake anatuluka, moti mzambayo anafuula kuti: “Ndiye chiyani wachitachi? Bwanji ukuchita kung’amba wekha njira?” N’chifukwa chake anamutcha dzina lakuti Perezi.*+
12 Ana a Yuda+ anali Ere,+ Onani,+ Shela,+ Perezi,+ ndi Zera.+ Komabe, Ere ndi Onani anafera kudziko la Kanani.+ Ana a Perezi anali Hezironi+ ndi Hamuli.+
3 Yuda anabereka Perezi+ ndi Zera, ndipo mayi awo anali Tamara.Perezi anabereka Hezironi.+Hezironi anabereka Ramu.+