Genesis 46:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Yuda+ anali Ere,+ Onani,+ Shela,+ Perezi,+ ndi Zera.+ Komabe, Ere ndi Onani anafera kudziko la Kanani.+ Ana a Perezi anali Hezironi+ ndi Hamuli.+ Numeri 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ana aamuna a Perezi anali Hezironi+ amene anali kholo la banja la Ahezironi, ndi Hamuli+ amene anali kholo la banja la Ahamuli. 1 Mbiri 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ana a Perezi anali Hezironi ndi Hamuli.+
12 Ana a Yuda+ anali Ere,+ Onani,+ Shela,+ Perezi,+ ndi Zera.+ Komabe, Ere ndi Onani anafera kudziko la Kanani.+ Ana a Perezi anali Hezironi+ ndi Hamuli.+
21 Ana aamuna a Perezi anali Hezironi+ amene anali kholo la banja la Ahezironi, ndi Hamuli+ amene anali kholo la banja la Ahamuli.