Genesis 38:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Ere, mwana woyamba wa Yuda, anakhala munthu woipa pamaso pa Yehova.+ Chotero Yehova anamupha.+ Genesis 38:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zimene anachitazo zinamuipira Yehova,+ chotero nayenso anamupha.+
7 Koma Ere, mwana woyamba wa Yuda, anakhala munthu woipa pamaso pa Yehova.+ Chotero Yehova anamupha.+