2 Samueli 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo mkwiyo wa Yehova+ unayakira Uza ndipo Mulungu woona anamukantha+ pomwepo chifukwa cha kuchita chinthu chosalemekeza Mulungu chimenechi. Moti Uza anafera pomwepo, pafupi ndi likasa la Mulungu woona.+ Machitidwe 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Nthawi yomweyo mngelo wa Yehova anamukantha,+ chifukwa sanapereke ulemerero kwa Mulungu.+ Ndipo anadyedwa ndi mphutsi n’kumwalira.
7 Pamenepo mkwiyo wa Yehova+ unayakira Uza ndipo Mulungu woona anamukantha+ pomwepo chifukwa cha kuchita chinthu chosalemekeza Mulungu chimenechi. Moti Uza anafera pomwepo, pafupi ndi likasa la Mulungu woona.+
23 Nthawi yomweyo mngelo wa Yehova anamukantha,+ chifukwa sanapereke ulemerero kwa Mulungu.+ Ndipo anadyedwa ndi mphutsi n’kumwalira.