Yesaya 42:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ine ndine Yehova. Dzina langa ndi limeneli,+ ndipo sindidzapereka ulemu wanga kwa wina aliyense+ kapena kupereka ulemerero wanga+ kwa zifaniziro zogoba.+ 1 Akorinto 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 kuti pasapezeke munthu wodzitama+ pamaso pa Mulungu.
8 “Ine ndine Yehova. Dzina langa ndi limeneli,+ ndipo sindidzapereka ulemu wanga kwa wina aliyense+ kapena kupereka ulemerero wanga+ kwa zifaniziro zogoba.+