Yesaya 48:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndithu, ndidzachitapo kanthu chifukwa cha dzina langa.+ Pakuti munthu angalekerere bwanji dzina lake likuipitsidwa?+ Ulemerero wanga sindidzaupereka kwa wina aliyense.+
11 Ndithu, ndidzachitapo kanthu chifukwa cha dzina langa.+ Pakuti munthu angalekerere bwanji dzina lake likuipitsidwa?+ Ulemerero wanga sindidzaupereka kwa wina aliyense.+