Deuteronomo 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ndipo aziuza akulu a mzindawo kuti, ‘Mwana wathuyu ndi wosamvera ndiponso ndi wopanduka. Iye samvera mawu athu+ ndipo ndi wosusuka+ ndiponso ndi chidakwa.’+ Agalatiya 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano, ntchito za thupi zimaonekera.+ Ntchitozi ndizo dama,*+ zinthu zodetsa, khalidwe lotayirira,+ 1 Petulo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti maso+ a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva pembedzero lawo,+ koma nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa.”+
20 ndipo aziuza akulu a mzindawo kuti, ‘Mwana wathuyu ndi wosamvera ndiponso ndi wopanduka. Iye samvera mawu athu+ ndipo ndi wosusuka+ ndiponso ndi chidakwa.’+
19 Tsopano, ntchito za thupi zimaonekera.+ Ntchitozi ndizo dama,*+ zinthu zodetsa, khalidwe lotayirira,+
12 Pakuti maso+ a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva pembedzero lawo,+ koma nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa.”+