Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 5:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 M’kalata yanga ndinakulemberani kuti muleke kuyanjana ndi anthu adama.

  • Aefeso 5:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Dama*+ ndi chonyansa chamtundu uliwonse kapena umbombo+ zisatchulidwe n’komwe pakati panu,+ monga mmene anthu oyera amayenera kuchitira.+

  • Akolose 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Choncho chititsani ziwalo za thupi+ lanu padziko lapansi kukhala zakufa+ ku dama, zinthu zodetsa, chilakolako cha kugonana,+ chikhumbo choipa, ndi kusirira kwa nsanje,+ kumene ndiko kulambira mafano.

  • Chivumbulutso 2:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “‘Komabe, ndakupeza ndi mlandu uwu. Walekerera mayi uja Yezebeli,+ amene amadzitcha mneneri. Iye amaphunzitsa+ ndi kusocheretsa akapolo anga+ kuti azichita dama+ ndi kudya zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena