Machitidwe 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 kupitiriza kupewa zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano,+ magazi,+ zopotola,+ ndi dama.+ Mukamapewa zinthu zimenezi mosamala kwambiri,+ zinthu zidzakuyenderani bwino. Tikukufunirani zabwino zonse!” 1 Akorinto 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma tsopano ndikukulemberani kuti muleke kuyanjana+ ndi aliyense wotchedwa m’bale, amene ndi wadama, kapena waumbombo,+ kapena wopembedza mafano, wolalata, chidakwa,+ kapena wolanda, ngakhale kudya naye munthu wotereyu ayi. Agalatiya 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano, ntchito za thupi zimaonekera.+ Ntchitozi ndizo dama,*+ zinthu zodetsa, khalidwe lotayirira,+ Aefeso 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti mfundo iyi mukuidziwa, ndipo mukuimvetsa bwino, kuti wadama+ kapena wodetsedwa kapena waumbombo,+ umene ndiwo kupembedza mafano, sadzalowa mu ufumu wa Khristu ndi wa Mulungu.+
29 kupitiriza kupewa zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano,+ magazi,+ zopotola,+ ndi dama.+ Mukamapewa zinthu zimenezi mosamala kwambiri,+ zinthu zidzakuyenderani bwino. Tikukufunirani zabwino zonse!”
11 Koma tsopano ndikukulemberani kuti muleke kuyanjana+ ndi aliyense wotchedwa m’bale, amene ndi wadama, kapena waumbombo,+ kapena wopembedza mafano, wolalata, chidakwa,+ kapena wolanda, ngakhale kudya naye munthu wotereyu ayi.
19 Tsopano, ntchito za thupi zimaonekera.+ Ntchitozi ndizo dama,*+ zinthu zodetsa, khalidwe lotayirira,+
5 Pakuti mfundo iyi mukuidziwa, ndipo mukuimvetsa bwino, kuti wadama+ kapena wodetsedwa kapena waumbombo,+ umene ndiwo kupembedza mafano, sadzalowa mu ufumu wa Khristu ndi wa Mulungu.+