Deuteronomo 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ndipo aziuza akulu a mzindawo kuti, ‘Mwana wathuyu ndi wosamvera ndiponso ndi wopanduka. Iye samvera mawu athu+ ndipo ndi wosusuka+ ndiponso ndi chidakwa.’+ 1 Akorinto 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 akuba, aumbombo,+ zidakwa,+ olalata, kapena olanda, onsewo sadzalowa mu ufumu wa Mulungu.+ Agalatiya 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 kaduka, kumwa mwauchidakwa,*+ maphwando aphokoso, ndi zina zotero. Ponena za zinthu zimenezi, ndikukuchenjezeranitu, ngati mmene ndinachitira poyamba paja, kuti anthu amene amachita zimenezi+ sadzalowa mu ufumu wa Mulungu.+ 1 Petulo 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti nthawi+ imene yapitayi inali yokwanira kwa inu kuchita chifuniro cha anthu a m’dzikoli+ pamene munali kuchita zinthu zosonyeza khalidwe lotayirira,+ zilakolako zoipa, kumwa vinyo mopitirira muyezo,+ maphwando aphokoso, kumwa kwa mpikisano, ndi kupembedza mafano kosaloleka.+
20 ndipo aziuza akulu a mzindawo kuti, ‘Mwana wathuyu ndi wosamvera ndiponso ndi wopanduka. Iye samvera mawu athu+ ndipo ndi wosusuka+ ndiponso ndi chidakwa.’+
21 kaduka, kumwa mwauchidakwa,*+ maphwando aphokoso, ndi zina zotero. Ponena za zinthu zimenezi, ndikukuchenjezeranitu, ngati mmene ndinachitira poyamba paja, kuti anthu amene amachita zimenezi+ sadzalowa mu ufumu wa Mulungu.+
3 Pakuti nthawi+ imene yapitayi inali yokwanira kwa inu kuchita chifuniro cha anthu a m’dzikoli+ pamene munali kuchita zinthu zosonyeza khalidwe lotayirira,+ zilakolako zoipa, kumwa vinyo mopitirira muyezo,+ maphwando aphokoso, kumwa kwa mpikisano, ndi kupembedza mafano kosaloleka.+