Aheberi 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yesetsani kukhala pa mtendere ndi anthu onse,+ komanso yesetsani kukhala oyera+ chifukwa ngati munthu si woyera, sadzaona Ambuye.+ 1 Petulo 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Ndipo ngati munthu wolungama adzapulumuka movutikira,+ kodi munthu wosaopa Mulungu ndi wochimwa adzaoneka n’komwe?”+
14 Yesetsani kukhala pa mtendere ndi anthu onse,+ komanso yesetsani kukhala oyera+ chifukwa ngati munthu si woyera, sadzaona Ambuye.+
18 “Ndipo ngati munthu wolungama adzapulumuka movutikira,+ kodi munthu wosaopa Mulungu ndi wochimwa adzaoneka n’komwe?”+