Mateyu 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Odala ndi anthu oyera mtima,+ chifukwa adzaona Mulungu.+ Aroma 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho, otsatira zofuna za thupi+ sangakondweretse Mulungu.